Ahebri 12:12 - Buku Lopatulika12 Mwa ichi limbitsani manja ogooka, ndi maondo olobodoka; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Mwa ichi limbitsani manja ogooka, ndi maondo olobodoka; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Limbitsani tsono manja anu ofooka ndiponso maondo anu agooka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Nʼchifukwa chake limbitsani manja anu otopa ndi mawondo anu ogowoka. Onani mutuwo |