Ahebri 11:21 - Buku Lopatulika21 Ndi chikhulupiriro Yakobo, poti alinkufa, anadalitsa yense wa ana a Yosefe; napembedza potsamira pamutu wa ndodo yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndi chikhulupiriro Yakobo, poti alinkufa, anadalitsa yense wa ana a Yosefe; napembedza potsamira pa mutu wa ndodo yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Pokhala ndi chikhulupiriro, Yakobe pakufa, adadalitsa ana a Yosefe mmodzimmodzi. Pochita zimenezi anali atayedzamira pa ndodo yake, akupembedza Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Ndi chikhulupiriro, pamene Yakobo ankamwalira anadalitsa ana awiri a Yosefe, ndipo anapembedza Mulungu atatsamira ndodo yake. Onani mutuwo |