Ahebri 11:22 - Buku Lopatulika22 Ndi chikhulupiriro, Yosefe, pakumwalira, anatchula za matulukidwe a ana a Israele; nalamulira za mafupa ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndi chikhulupiriro, Yosefe, pakumwalira, anatchula za matulukidwe a ana a Israele; nalamula za mafupa ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Pokhala ndi chikhulupiriro, Yosefe ali pafupi kutsirizika, adanenapo za kutuluka kwa Aisraele mu Ejipito, naŵauziratu za m'mene adaayenera kudzachitira ndi mafupa ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ndi chikhulupiriro Yosefe ali pafupi kumwalira anayankhula za kutuluka kwa Aisraeli mu Igupto ndipo anawawuza zoti adzachite ndi mafupa ake. Onani mutuwo |