Ahebri 11:20 - Buku Lopatulika20 Ndi chikhulupiriro Isaki anadalitsa Yakobo ndi Esau, zingakhale za zinthu zilinkudza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndi chikhulupiriro Isaki anadalitsa Yakobo ndi Esau, zingakhale za zinthu zilinkudza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Pokhala ndi chikhulupiriro, Isaki adapemphera ana ake, Yakobe ndi Esau, madalitso am'tsogolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Ndi chikhulupiriro Isake anadalitsa Yakobo ndi Esau pa zatsogolo lawo. Onani mutuwo |