Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Ahebri 10:9 - Buku Lopatulika

9 pamenepo anati, Taonani, ndafika kudzachita chifuniro chanu. Achotsa choyambacho, kuti akaike chachiwiricho.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 pamenepo anati, Taonani, ndafika kudzachita chifuniro chanu. Achotsa choyambacho, kuti akaike chachiwiricho.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Koma pambuyo pake adati, “Ndabweratu, kuti ndichite zimene mukufuna.” Motero Khristu adathetsa mphamvu za nsembe za mtundu woyamba zija, kuti m'malo mwake akhazikitse nsembe ya mtundu wachiŵiriyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Pamenepo Iye anati, “Ndili pano Ine, ndabwera kudzachita zimene mukufuna.” Khristu anachotsa nsembe zoyamba zija kuti mʼmalo mwake ayikemo nsembe za mtundu wachiwiri.

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 10:9
7 Mawu Ofanana  

Pamenepo ndinati, Taonani, ndadza; m'buku mwalembedwa za Ine,


kuchita chikondwero chanu kundikonda, Mulungu wanga; ndipo malamulo anu ali m'kati mwamtima mwanga.


pamenepo ndinati, Taonani, ndafika, (Pamutu pake pa buku palembedwa za Ine) kudzachita chifuniro chanu, Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa