Ahebri 10:7 - Buku Lopatulika7 pamenepo ndinati, Taonani, ndafika, (Pamutu pake pa buku palembedwa za Ine) kudzachita chifuniro chanu, Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 pamenepo ndinati, Taonani, ndafika, (Pamutu pake pa buku palembedwa za Ine) kudzachita chifuniro chanu, Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tsono ine ndidati, ‘Inu Mulungu, ndabweratu kuti ndichite zimene mukufuna, paja zidalembedwa choncho ponena za Ine m'buku la Malamulo.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Tsono, Ine ndinati, ‘Ndili pano Ine, Inu Mulungu, ndabwera kudzachita zimene mukufuna monga zinalembedwa mʼMalemba.’ ” Onani mutuwo |