Ahebri 10:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti sikutheka kuti mwazi wa ng'ombe zamphongo, ndi mbuzi ukachotsera machimo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti sikutheka kuti mwazi wa ng'ombe zamphongo, ndi mbuzi ukachotsera machimo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Magazi a ng'ombe zamphongo ndi a atonde sangathe konse kuchotsa machimo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Chifukwa nʼkosatheka kuti magazi angʼombe yayimuna ndi mbuzi yayimuna achotse machimo. Onani mutuwo |