Ahebri 10:3 - Buku Lopatulika3 Komatu mu izizo muli chikumbukiro cha machimo chaka ndi chaka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Komatu mu izizo muli chikumbukiro cha machimo chaka ndi chaka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Koma monga zilirimu, nsembezo zimakumbutsa anthu za machimo ao chaka ndi chaka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Koma nsembezo zimawakumbutsa anthuwo machimo awo chaka ndi chaka. Onani mutuwo |