Ahebri 10:18 - Buku Lopatulika18 Koma pomwe pali chikhululukiro cha machimo palibenso chopereka cha kwa uchimo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Koma pomwe pali chikhululukiro cha machimo palibenso chopereka cha kwa uchimo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pamene Mulungu wakhululukira zonsezi, sipafunikanso nsembe yoperekera machimo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndipo pamene machimo akhululukidwa, sipafunikanso nsembe yoperekedwa chifukwa cha machimowo. Onani mutuwo |