Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Ahebri 10:17 - Buku Lopatulika

17 ndipo machimo ao ndi kusaweruzika kwao sindidzakumbukiranso.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 ndipo machimo ao ndi masaweruziko ao sindidzawakumbukiranso.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Pambuyo pake akutinso, “Sindidzaŵakumbukiranso konse machimo ao ndi zolakwa zao.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Ndipo akutinso: “Sindidzakumbukiranso konse machimo awo ndi zolakwa zawo.”

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 10:17
4 Mawu Ofanana  

Taonani masiku adza, ati Yehova, ndipo ndidzapangana pangano latsopano ndi nyumba ya Israele, ndi nyumba ya Yuda;


ndipo sadzaphunzitsa yense mnansi wake, ndi yense mbale wake, kuti, Mudziwe Yehova; pakuti iwo onse adzandidziwa, kuyambira wamng'ono kufikira wamkulu wa iwo, ati Yehova; pakuti ndidzakhululukira mphulupulu yao, ndipo sindidzakumbukira tchimo lao.


Koma pomwe pali chikhululukiro cha machimo palibenso chopereka cha kwa uchimo.


Kuti ndidzachitira chifundo zosalungama zao, ndipo zoipa zao sindidzazikumbukanso.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa