Afilipi 4:14 - Buku Lopatulika14 Koma munachita bwino kuti munayanjana nane m'chisautso changa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Koma munachita bwino kuti munayanjana nane m'chisautso changa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Komabe mudaachita bwino kundithandiza pa zovuta zanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Komatu munachita bwino kundithandiza mʼmavuto anga. Onani mutuwo |