Afilipi 4:13 - Buku Lopatulika13 Ndikhoza zonse mwa Iye wondipatsa mphamvuyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndikhoza zonse mwa Iye wondipatsa mphamvuyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ndingathe kuchita zonse chifukwa Khristu amandipatsa mphamvu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ndikhoza kuchita zonse kudzera mwa Iye amene amandipatsa mphamvu. Onani mutuwo |