Afilipi 3:7 - Buku Lopatulika7 Komatu zonse zimene zinandipindulira, zomwezo ndinaziyesa chitayiko chifukwa cha Khristu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Komatu zonse zimene zinandipindulira, zomwezo ndinaziyesa chitayiko chifukwa cha Khristu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Koma chifukwa cha Khristu, zomwe kale ndinkaziyesa zaphindu, tsopano ndikuziwona kuti nzosapindula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma zonse zimene ndinkaziyesa zaphindu, tsopano ndikuziona kuti nʼzosapindulitsa chifukwa cha Khristu. Onani mutuwo |