Afilipi 2:4 - Buku Lopatulika4 munthu yense asapenyerere zake za iye yekha, koma yense apenyererenso za mnzake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 munthu yense asapenyerere zake za iye yekha, koma yense apenyererenso za mnzake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Musamangofuna zokomera inu nokha, koma zokomeranso anzanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Musamangofuna zokomera inu nokha koma aliyense azifuna zokomeranso ena. Onani mutuwo |