Afilipi 1:8 - Buku Lopatulika8 Pakuti Mulungu ali mboni yanga, kuti ndilakalaka inu nonse m'phamphu la mwa Khristu Yesu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pakuti Mulungu ali mboni yanga, kuti ndilakalaka inu nonse m'phamphu la mwa Khristu Yesu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mulungu akundichitira umboni kuti ndimakulakalakani kwambiri, pakuti ndimakukondani ndi mtima wonse, motsanzira chikondi cha Khristu Yesu mwini. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mulungu angandichitire umboni kuti ndimakulakalakani ndi chikondi cha Khristu Yesu. Onani mutuwo |