Afilipi 1:29 - Buku Lopatulika29 kuti kwapatsidwa kwa inu kwaufulu chifukwa cha Khristu, si kukhulupirira kwa Iye kokha, komatunso kumva zowawa chifukwa cha Iye, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 kuti kwapatsidwa kwa inu kwaufulu chifukwa cha Khristu, si kukhulupirira kwa Iye kokha, komatunso kumva zowawa chifukwa cha Iye, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Paja Iye adakupatsani mwai, osati wakungokhulupirira Khristu ai, komanso wakumva zoŵaŵa chifukwa cha Iye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Pakuti inu mwapatsidwa mwayi osati ongokhulupirira Khristu kokha, koma wakumva zowawa mʼmalo mwa Khristu. Onani mutuwo |