Afilipi 1:30 - Buku Lopatulika30 ndi kukhala nacho inu chilimbano chomwechi mudachiona mwa ine, nimukumva tsopano chili mwa ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 ndi kukhala nacho inu chilimbano chomwechi mudachiona mwa ine, nimukumva tsopano chili mwa ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Inunso mukumenya nkhondo yomwe ija imene mudandiwona ine ndikuimenya, yomwenso ndikumenyabe tsopano, monga mukumveramu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Inunso mukudutsa mʼzowawa zomwe zija munaona ndikudutsamo inenso ndipo pano mukumva kuti ndikukumana nazobe. Onani mutuwo |