Afilipi 1:16 - Buku Lopatulika16 ena atero ndi chikondi, podziwa kuti anandiika ndichite chokanira cha Uthenga Wabwino; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 ena atero ndi chikondi, podziwa kuti anandiika ndichite chokanira cha Uthenga Wabwino; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Otsirizaŵa amamlalika chifukwa cha chikondi, popeza kuti amadziŵa kuti Mulungu adandikhazika muno kuti ndigwire ntchito yoteteza Uthenga Wabwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Olalikira ndi zolinga zabwinowa amachita izi mwachikondi, podziwa kuti ine ndili muno chifukwa cha kuteteza Uthenga Wabwino. Onani mutuwo |