Afilipi 1:14 - Buku Lopatulika14 ndi kuti unyinji wa abale mwa Ambuye, pokhulupirira m'zomangira zanga, alimbika mtima koposa kulankhula mau a Mulungu opanda mantha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 ndi kuti unyinji wa abale mwa Ambuye, pokhulupirira m'zomangira zanga, alimbika mtima koposa kulankhula mau a Mulungu opanda mantha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono chifukwa choti ndili m'ndende, abale ochuluka akulimba mtima mwa Ambuye, ndipo akulalika mau a Mulungu mopanda mantha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Moti chifukwa cha maunyolo angawa, abale ambiri alimbikitsidwa kuyankhula Mawu a Mulungu molimbika ndi mopanda mantha. Onani mutuwo |