Afilipi 1:13 - Buku Lopatulika13 kotero kuti zomangira zanga zinaonekera mwa Khristu m'bwalo lonse la alonda, ndi kwa ena onse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 kotero kuti zomangira zanga zinaonekera mwa Khristu m'bwalo lonse la alonda, ndi kwa onse ena; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mwakuti asilikali onse olonda nyumba ya mfumu, ndi ena onse kuno, adziŵa kuti ndili m'ndende chifukwa cha Khristu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Chotsatira chake nʼchakuti zadziwika bwino lomwe kwa onse amene ali ku nyumba yaufumu kuti ine ndili mʼmaunyolo chifukwa cha Khristu. Onani mutuwo |