Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Aefeso 5:12 - Buku Lopatulika

12 pakuti zochitidwa nao m'tseri, kungakhale kuzinena kuchititsa manyazi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 pakuti zochitidwa nao m'tseri, kungakhale kuzinena kuchititsa manyazi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Paja zimene iwo amachita mobisa, ngakhale kuzitchula komwe kumachititsa manyazi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Pakuti ndi zochititsa manyazi ngakhale kutchula zomwe zimachitika mseri.

Onani mutuwo Koperani




Aefeso 5:12
12 Mawu Ofanana  

Pakuti iwe unachichita m'tseri; koma Ine ndidzachita chinthu ichi pamaso pa Aisraele onse, dzuwa lili nde.


madzi akuba atsekemera, ndi chakudya chobisika chikoma.


Pakuti Mulungu adzanena mlandu wa zochita zonse, ndi zobisika zonse, ngakhale zabwino ngakhale zoipa.


Kodi munthu angathe kubisala mobisika kuti ndisamuone iye? Ati Yehova. Kodi Ine sindidzala kumwamba ndi dziko lapansi? Ati Yehova.


tsiku limene Mulungu adzaweruza ndi Khristu Yesu zinsinsi za anthu, monga mwa Uthenga wanga Wabwino.


ndipo musayanjane nazo ntchito za mdima zosabala kanthu, koma makamakanso muzitsutse;


Koma zinthu zonse potsutsika ndi kuunika, zionekera; pakuti chonse chakuonetsa chili kuunika.


Koma dama ndi chidetso chonse, kapena chisiriro, zisatchulidwe ndi kutchulidwa komwe mwa inu, monga kuyenera oyera mtima;


Pakuti nthawi yapitayi idakufikirani kuchita chifuniro cha amitundu, poyendayenda inu m'kukhumba zonyansa, zilakolako, maledzero, madyerero, maimwaimwa, ndi kupembedza mafano kosaloleka;


Ndipo ndinaona akufa, aakulu ndi aang'ono alinkuima kumpando wachifumu; ndipo mabuku anatsegulidwa; ndipo buku lina linatsegulidwa, ndilo la moyo; ndipo akufa anaweruzidwa mwa zolembedwa m'mabuku, monga mwa ntchito zao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa