Aefeso 5:11 - Buku Lopatulika11 ndipo musayanjane nazo ntchito za mdima zosabala kanthu, koma makamakanso muzitsutse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 ndipo musayanjane nazo ntchito za mdima zosabala kanthu, koma makamakanso muzitsutse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Musayanjane nawo anthu ochita zopanda pake za mdima, koma muŵatsutse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Musayanjane nazo ntchito zosapindulitsa za mdima, koma mʼmalo mwake muzitsutse. Onani mutuwo |