Aefeso 5:10 - Buku Lopatulika10 kuyesera chokondweretsa Ambuye nchiyani; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 kuyesera chokondweretsa Ambuye nchiyani; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Muziyesa kudziŵa kwenikweni zimene zingakondweretse Ambuye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Inu mufufuze chimene chimakondweretsa Ambuye. Onani mutuwo |