Aefeso 4:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo kwa yense wa ife chapatsika chisomo, monga mwa muyeso wa mphatso ya Khristu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo kwa yense wa ife chapatsika chisomo, monga mwa muyeso wa mphatso ya Khristu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Komabe aliyense wa ife adalandira mphatso yakeyake yaulere, molingana ndi m'mene Khristu amaperekera mphatso zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma aliyense wa ife wapatsidwa chisomo molingana ndi muyeso wa mphatso ya Khristu. Onani mutuwo |