Aefeso 4:22 - Buku Lopatulika22 kuti muvule, kunena za makhalidwe anu oyamba, munthu wakale, wovunda potsata zilakolako za chinyengo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 kuti muvule, kunena za makhalidwe anu oyamba, munthu wakale, wovunda potsata zilakolako za chinyengo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Mudaphunzira kuti muleke mayendedwe anu akale, muvule moyo wanu wakale uja umene unkadziwononga ndi zilakolako zake zonyenga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Inu munaphunzitsidwa molingana ndi moyo wanu wakale, kuchotsa umunthu wakale, umene ukupitirira kuwonongeka ndi zilakolako zachinyengo; Onani mutuwo |