Aefeso 3:3 - Buku Lopatulika3 ndi umo anandizindikiritsa chinsinsicho mwa vumbulutso, monga ndinalemba kale mwachidule, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndi umo anandizindikiritsa chinsinsicho mwa vumbulutso, monga ndinalemba kale mwachidule, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Adandiwululira chinsinsi chake, monga ndidakulemberani mwachidule posachedwapa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 ndicho chinsinsi chimene chinawululidwa kwa ine mwa vumbulutso, monga ndinakulemberani kale mwachidule. Onani mutuwo |