Aefeso 3:13 - Buku Lopatulika13 Mwa ichi ndipempha kuti musade mtima m'zisautso zanga chifukwa cha inu, ndiwo ulemerero wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Mwa ichi ndipempha kuti musade mtima m'zisautso zanga chifukwa cha inu, ndiwo ulemerero wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ndikukupemphani tsono kuti musataye mtima chifukwa chakuti ndikukusaukirani. Kwenikweni muyenera kunyadira chifukwa cha kusauka kwangaku. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Choncho, ine ndikukupemphani kuti musakhumudwe popeza ndikusautsidwa chifukwa cha inu pakuti masautso angawa ndi ulemerero wanu. Onani mutuwo |