Aefeso 3:12 - Buku Lopatulika12 amene tili naye chokhazikika mtima ndi chiyandiko cholimbika, mwa chikhulupiriro cha pa Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 amene tili naye chokhazikika mtima ndi chiyandiko cholimbika, mwa chikhulupiriro cha pa Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Popeza kuti timakhulupirira Iyeyu, tingathe kulimba mtima kuyandikira kwa Mulungu mosakayika konse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Mwa Khristu ndi mwa chikhulupiriro chathu mwa Iye, timayandikira kwa Mulungu momasuka ndi molimbika mtima. Onani mutuwo |