Aefeso 2:17 - Buku Lopatulika17 ndipo m'mene anadza, analalikira Uthenga Wabwino wa mtendere kwa inu akutali, ndi mtendere kwa iwo apafupi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 ndipo m'mene anadza, analalikira Uthenga Wabwino wa mtendere kwa inu akutali, ndi mtendere kwa iwo apafupi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Khristu adadzalalika Uthenga Wabwino wa mtendere kwa inu a mitundu inanu, amene munali kutali ndi Mulungu, ndiponso kwa Ayuda, amene anali pafupi naye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Iye anabwera ndipo analalikira mtendere kwa inu amene munali kutali ndi mtendere ndiponso kwa iwonso amene anali pafupi. Onani mutuwo |