Aefeso 1:2 - Buku Lopatulika2 Chisomo kwa inu, ndi mtendere wochokera kwa Mulungu Atate wathu, ndi Ambuye Yesu Khristu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Chisomo kwa inu, ndi mtendere wochokera kwa Mulungu Atate wathu, ndi Ambuye Yesu Khristu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mulungu Atate athu ndi Ambuye Yesu Khristu akukomereni mtima ndi kukupatsani mtendere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Chisomo ndi mtendere kwa inu zochokera kwa Mulungu Atate athu ndi Ambuye Yesu Khristu. Onani mutuwo |