3 Yohane 1:8 - Buku Lopatulika8 Chifukwa chake ife tiyenera kulandira otere, kuti tikakhale othandizana nacho choonadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Chifukwa chake ife tiyenera kulandira otere, kuti tikakhale othandizana nacho choonadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono ife tiyenera kumaŵathandiza anthu otere, kuti tigwirizane nawo pa ntchito yofalitsa choona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ife tiyenera kumathandiza anthu oterewa, kuti tigwirizane nawo pa ntchito ya choonadi. Onani mutuwo |