3 Yohane 1:2 - Buku Lopatulika2 Wokondedwa, ndipemphera kuti pa zonse ulemere, nukhale bwino, monga mzimu wako ulemera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Wokondedwa, ndipemphera kuti pa zonse ulemere, nukhale bwino, monga mzimu wako ulemera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Wokondedwa, ndimapemphera kuti zako zonse zikuyendere bwino, ndipo kuti moyo wako wathupi ukhale wolimba, monga momwe uliri moyo wako wauzimu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Wokondedwa, ndimakupempherera kuti zako zonse zikuyendere bwino, ndikuti ukhale bwino mʼthupi mwako, monga momwe ulili moyo wako wauzimu. Onani mutuwo |