Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




3 Yohane 1:1 - Buku Lopatulika

1 Mkuluyo kwa Gayo wokondedwayo, amene ndikondana naye m'choonadi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Mkuluyo kwa Gayo wokondedwayo, amene ndikondana naye m'choonadi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Ine mkulune ndikulemba kalatayi kwa Gayo wokondedwa, amene ndimamkonda kwenikweni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Ndine mkulu wampingo, kulembera: Gayo mnzanga wokondedwa, amene ndimamukonda mʼchoonadi.

Onani mutuwo Koperani




3 Yohane 1:1
9 Mawu Ofanana  

ichonso anachita, natumiza kwa akulu mwa dzanja la Barnabasi ndi Saulo.


Ndipo m'mzinda monse munachita piringupiringu, nathamangira onse pamodzi ku bwalo losewera, atagwira Gayo ndi Aristariko, anthu a ku Masedoniya, alendo anzake a Paulo.


Ndipo anamperekeza kufikira ku Asiya Sopatere mwana wa Piro, wa ku Berea; ndipo a Atesalonika, Aristariko ndi Sekundo; ndi Gayo wa ku Deribe, ndi Timoteo; ndi a ku Asiya, Tikiko ndi Trofimo.


Gayo, mwini nyumba wolandira ine, ndi Mpingo wonse wa Ambuye, akupereka moni. Erasto, ndiye woyang'anira mzinda, akupereka moni, ndiponso Kwarto mbaleyo.


Ndiyamika Mulungu kuti sindinabatize mmodzi yense wa inu, koma Krispo ndi Gayo;


Akulu tsono mwa inu ndiwadandaulira, ine mkulu mnzanu ndi mboni ya zowawa za Khristu, ndinenso wolawana nao ulemerero udzavumbulutsikawo:


Tiana, tisakonde ndi mau, kapena ndi lilime, komatu ndi kuchita ndi m'choonadi.


Wokondedwa, ndipemphera kuti pa zonse ulemere, nukhale bwino, monga mzimu wako ulemera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa