Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Yohane 1:13 - Buku Lopatulika

13 Akupereka moni ana a mbale wanu wosankhika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Akupereka moni ana a mbale wanu wosankhika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Ana a mbale wanu wosankhidwa ndi Mulungu akuti moni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Ana a mlongo wanu wosankhidwa ndi Mulungu akupereka moni.

Onani mutuwo Koperani




2 Yohane 1:13
3 Mawu Ofanana  

Ndipo ngati mupatsa moni abale anu okhaokha, muchitanji choposa ena? Kodi angakhale anthu akunja sachita chomwecho?


Iye wa ku Babiloni wosankhidwa pamodzi nanu akukupatsani moni; ateronso Marko mwana wanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa