Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




3 Yohane 1:14 - Buku Lopatulika

14 koma ndiyembekeza kukuona iwe msanga, ndipo tidzalankhula popenyana.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 koma ndiyembekeza kukuona iwe msanga, ndipo tidzalankhula popenyana.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Ndikuyembekeza kudzakuwona posachedwa. Pamenepo tidzakambirana pakamwa mpakamwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Ndiyembekezera kufika kwanuko posachedwapa, ndipo tidzakambirana pamaso ndi pamaso.

Onani mutuwo Koperani




3 Yohane 1:14
10 Mawu Ofanana  

Ndipo iye anati, Mtendere ukhale ndi inu, musaope; Mulungu wanu ndi Mulungu wa atate wanu anakupatsani inu chuma m'matumba anu; ine ndinali nazo ndalama zanu. Pamenepo anawatulutsira Simeoni.


Mfumu Nebukadinezara, kwa anthu mitundu ya anthu, ndi a manenedwe okhala padziko lonse lapansi: Mtendere uchulukire inu.


Iyeyu, wapakhomo amtsegulira ndi nkhosa zimva mau ake; ndipo aitana nkhosa za iye yekha maina ao, nazitsogolera kunja.


Pamenepo, pokhala madzulo, tsiku lomwelo, loyamba la Sabata, makomo ali chitsekere, kumene anakhala ophunzira, chifukwa cha kuopa Ayuda, Yesu anadza naimirira pakati pao, nanena nao, Mtendere ukhale ndi inu.


Chifukwa chake Yesu anatinso kwa iwo, Mtendere ukhale ndi inu; monga Atate wandituma Ine, Inenso ndituma inu.


Koma ndinena, Muyendeyende ndi Mzimu, ndipo musafitse chilakolako cha thupi.


Mtendere ukhale kwa abale, ndi chikondi, pamodzi ndi chikhulupiriro, zochokera kwa Mulungu Atate, ndi Ambuye Yesu Khristu.


Mupatsane moni ndi kupsompsonana kwa chikondi. Mtendere ukhale ndi inu nonse muli mwa Khristu.


Pokhala ndili nazo zambiri zakukulemberani, sindifuna kuchita ndi kalata ndi kapezi; koma ndiyembekeza kudza kwa inu, ndi kulankhula popenyana, kuti chimwemwe chanu chikwanire.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa