Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




3 Yohane 1:13 - Buku Lopatulika

13 Ndinali nazo zambiri za kukulembera, komatu sindifuna kukulembera ndi kapezi ndi peni;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndinali nazo zambiri za kukulembera, komatu sindifuna kukulembera ndi kapezi ndi peni;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Ndinali ndi zambiri zoti ndikuuze, koma sindingakonde kuzilemba m'kalata.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Ndili ndi zambiri zoti ndikulembereni, koma sindikufuna kuzilemba mʼkalata.

Onani mutuwo Koperani




3 Yohane 1:13
2 Mawu Ofanana  

Koma Yosefe, mwamuna wake, anali wolungama, ndiponso sanafune kunyazitsa iye, nayesa m'mtima kumleka iye m'tseri.


Pokhala ndili nazo zambiri zakukulemberani, sindifuna kuchita ndi kalata ndi kapezi; koma ndiyembekeza kudza kwa inu, ndi kulankhula popenyana, kuti chimwemwe chanu chikwanire.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa