3 Yohane 1:15 - Buku Lopatulika15 Mtendere ukhale nawe. Akupereka moni abwenzi. Upereke moni kwa abwenzi ndi kutchula maina ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Mtendere ukhale nawe. Akupereka moni abwenzi. Upereke moni kwa abwenzi ndi kutchula maina ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Mtendere ukhale nawe. Abwenzi onse akuti moni. Uperekeko moni kwa abwenzi onse mmodzimmodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Mtendere ukhale nawe. Abwenzi anu kuno akupereka moni. Upereke moni kwa abwenzi onse mmodzimmodzi. Onani mutuwo |