2 Yohane 1:2 - Buku Lopatulika2 chifukwa cha choonadi chimene chikhala mwa ife, ndipo chidzakhala ndi ife ku nthawi yosatha: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 chifukwa cha choonadi chimene chikhala mwa ife, ndipo chidzakhala ndi ife ku nthawi yosatha: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Timakukondani chifukwa cha choona chimene chimakhala mwa ife, ndipo chidzakhala nafe mpaka muyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Timakukondani chifukwa cha choonadi chimene chimakhala mwa ife ndipo chidzakhala mwa ife mpaka muyaya. Onani mutuwo |