2 Timoteyo 2:4 - Buku Lopatulika4 Msilikali sakodwa nazo ntchito wamba, kuti akakondweretse iye amene adamlemba usilikali. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Msilikali sakodwa nazo ntchito wamba, kuti akakondweretse iye amene adamlemba usilikali. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Msilikali amene akumenya nkhondo sasamalako ntchito zakumudzi, chifukwa iye amangofuna kukondweretsa mkulu wa ankhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Palibe msilikali amene ali pa ntchito amagwiranso ntchito za anthu wamba, iye amafuna kukondweretsa bwana wolamulira. Onani mutuwo |