2 Timoteyo 2:3 - Buku Lopatulika3 Umve zowawa pamodzi nane monga msilikali wabwino wa Khristu Yesu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Umve zowawa pamodzi nane monga msilikali wabwino wa Khristu Yesu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Umve nao zoŵaŵa monga msilikali wabwino wa Khristu Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Umve nane zowawa, monga msilikali wa Khristu Yesu. Onani mutuwo |