2 Timoteyo 1:2 - Buku Lopatulika2 kwa Timoteo, mwana wanga wokondedwa: Chisomo, chifundo, mtendere za kwa Mulungu Atate ndi Khristu Yesu Ambuye wathu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 kwa Timoteo, mwana wanga wokondedwa: Chisomo, chifundo, mtendere za kwa Mulungu Atate ndi Khristu Yesu Ambuye wathu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ndikulembera iwe Timoteo, mwana wanga wokondedwa. Mulungu Atate ndi Khristu Yesu Ambuye athu akukomere mtima, akuchitire chifundo ndi kukupatsa mtendere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Kwa Timoteyo, mwana wanga wokondedwa: Chisomo, chifundo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate ndi Ambuye athu Yesu Khristu. Onani mutuwo |