2 Samueli 9:13 - Buku Lopatulika13 Chomwecho Mefiboseti anakhala ku Yerusalemu, pakuti anadya masiku onse ku gome la mfumu, ndipo anali wopunduka mapazi ake onse awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Chomwecho Mefiboseti anakhala ku Yerusalemu, pakuti anadya masiku onse ku gome la mfumu, ndipo anali wopunduka mapazi ake onse awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Choncho Mefibosetiyo adakhala ku Yerusalemu, poti iyeyo ankadya ku nyumba ya mfumu masiku onse. Koma tsono anali wolumala mapazi onse aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ndipo Mefiboseti anakhala mu Yerusalemu chifukwa nthawi zonse amadya ndi mfumu. Iye anali wolumala mapazi ake onse. Onani mutuwo |