Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 9:12 - Buku Lopatulika

12 Ndipo Mefiboseti anali ndi mwana wamwamuna wamng'ono, dzina lake ndiye Mika. Ndipo onse akukhala m'nyumba ya Ziba anali anyamata a Mefiboseti.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndipo Mefiboseti anali ndi mwana wamwamuna wamng'ono, dzina lake ndiye Mika. Ndipo onse akukhala m'nyumba ya Ziba anali anyamata a Mefiboseti.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Mefiboseti anali ndi mwana wamng'ono, dzina lake Mika. Ndipo anthu onse amene ankakhala m'nyumba ya Ziba, adasanduka atumiki a Mefiboseti.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Mefiboseti anali ndi mwana wamngʼono wamwamuna wotchedwa Mika, ndipo onse a banja la Ziba anali antchito a Mefiboseti.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 9:12
8 Mawu Ofanana  

Pomwepo Ziba anati kwa mfumu, Monga mwa zonse mfumu mbuye wanga mulamulira mnyamata wanu, momwemo adzachita mnyamata wanu. Tsono Mefiboseti, anadya pa gome la Davide monga wina wa ana a mfumu.


Chomwecho Mefiboseti anakhala ku Yerusalemu, pakuti anadya masiku onse ku gome la mfumu, ndipo anali wopunduka mapazi ake onse awiri.


Ndipo Saharaimu anabala ana ku dziko la Mowabu, atachotsa akazi ake Husimu ndi Baara.


Mika, Rehobu, Hasabiya,


ndi Mataniya mwana wa Mika, mwana wa Zabidi, mwana wa Asafu, ndiye mkulu wakuyamba mayamiko, popemphera; ndi Bakibukiya wotsatana naye mwa abale ake, ndi Abida mwana wa Samuwa, mwana wa Galali, mwana wa Yedutuni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa