2 Samueli 10:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo kunali zitapita izi, mfumu ya ana a Amoni inamwalira, ndipo Hanuni mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo kunali zitapita izi, mfumu ya ana a Amoni inamwalira, ndipo Hanuni mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pambuyo pake Nahasi mfumu ya Aamoni adamwalira, ndipo Hanuni mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Patapita nthawi, mfumu ya Aamoni inamwalira, ndipo mwana wake Hanuni analowa ufumu mʼmalo mwake. Onani mutuwo |