2 Samueli 8:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo ku Beta ndi ku Berotai mizinda ya Hadadezere, mfumu Davide anatenga mikuwa yambiri ndithu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo ku Beta ndi ku Berotai midzi ya Hadadezere, mfumu Davide anatenga mikuwa yambiri ndithu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Kuchokera ku Beta ndi ku Berotai, mizinda ya Hadadezere, Mfumu Davide adabwerako ndi mkuŵa wambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mfumu Davide inatenga mkuwa wambiri kuchokera ku Beta ndi Berotai, mizinda ya Hadadezeri. Onani mutuwo |