Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 8:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo pamene Toi mfumu ya ku Hamati anamva kuti Davide adakantha khamu lonse la Hadadezere,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo pamene Toi mfumu ya ku Hamati anamva kuti Davide adakantha khamu lonse la Hadadezere,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Pamene Toi mfumu ya ku Hamati adamva kuti Davide wagonjetsa gulu lonse lankhondo la Hadadezere,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Tou, mfumu ya Hamati atamva kuti Davide wagonjetsa gulu lonse lankhondo la Hadadezeri,

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 8:9
6 Mawu Ofanana  

Toi anatumiza mwana wake Yoramu kwa mfumu Davide, kuti akamlonjere ndi kumdalitsa, popeza anamenyana ndi Hadadezere ndi kumkantha; pakuti pakati pa Hadadezere ndi Toi panali nkhondo. Ndipo Yoramu anabwera ndi zotengera zasiliva, ndi zotengera zagolide, ndi zotengera zamkuwa.


Ndipo nthawi yomweyo Solomoni anachita madyerero pamaso pa Yehova Mulungu wathu, ndi Israele yense pamodzi naye, msonkhano waukulu wakuyambira polowera ku Hamati kufikira ku nyanja ya ku Ejipito, masiku asanu ndi awiri, ndi masiku asanu ndi awiri ena, ndiwo masiku khumi mphambu anai.


Ndipo pakumva Tou, mfumu ya ku Hamati, kuti Davide adakantha khamu lonse la Hadadezere mfumu ya ku Zoba,


Ndipo anamanga Tadimori m'chipululu, ndi mizinda yonse yosungiramo chuma, imene anaimanga mu Hamati.


Pitani ku Kaline, nimuone; kuchokera komweko mupite ku Hamati wamkulu mutsikire ku Gati wa Afilisti; kodi awo ndi okoma koposa maufumu ano? Kapena malire ao aposa malire anu?


kuchokera kuphiri la Hori mulinge polowera Hamati; ndipo kutuluka kwake kwa malire kudzakhala ku Zedadi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa