2 Samueli 8:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Davide anatenga zikopa zagolide zinali ndi anyamata a Hadadezere, nabwera nazo ku Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Davide anatenga zikopa zagolide zinali ndi anyamata a Hadadezere, nabwera nazo ku Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Davide adatenga zishango zagolide zimene anyamata a Hadadezere ankanyamula, nabwera nazo ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Davide anatenga zishango zagolide za akuluakulu ankhondo a Hadadezeri ndi kubwera nazo ku Yerusalemu. Onani mutuwo |