2 Samueli 8:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Benaya mwana wa Yehoyada anayang'anira Akereti ndi Apeleti. Ndipo ana a Davide anali ansembe ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Benaya mwana wa Yehoyada anayang'anira Akereti ndi Apeleti. Ndipo ana a Davide anali ansembe ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Benaya, mwana wa Yehoyada, anali nduna yoyang'anira Akereti ndi Apeleti, ndipo ana a Davide anali ansembe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Benaya mwana wa Yehoyada anali mtsogoleri wa Akereti ndi Apeleti; ndipo ana a Davide anali ansembe. Onani mutuwo |