2 Samueli 8:17 - Buku Lopatulika17 ndi Zadoki mwana wa Ahitubi, ndi Ahimeleki mwana wa Abiyatara anali ansembe, ndi Seraya anali mlembi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 ndi Zadoki mwana wa Ahitubi, ndi Ahimeleki mwana wa Abiyatara anali ansembe, ndi Seraya anali mlembi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Zadoki, mwana wa Ahitubi, ndiponso Ahimeleki, mwana wa Abiyatara, anali ansembe, ndipo Seraya anali mlembi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Zadoki mwana wa Ahitubi ndi Ahimeleki mwana wa Abiatara anali ansembe; Seraya anali mlembi; Onani mutuwo |