2 Samueli 9:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Davide anati, Kodi atsalako wina wa nyumba ya Saulo, kuti ndimchitire chifundo chifukwa cha Yonatani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Davide anati, Kodi atsalako wina wa nyumba ya Saulo, kuti ndimchitire chifundo chifukwa cha Yonatani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsiku lina Davide adafunsa kuti, “Kodi alipo wina aliyense wa banja la Saulo amene adatsalako? Ndikufuna kuti ndimchitire chifundo chifukwa cha Yonatani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Davide anafunsa kuti, “Kodi alipo amene watsala mʼbanja la Sauli kuti ndimuchitire chifundo chifukwa cha Yonatani?” Onani mutuwo |